Testo Akumbutseni - Emmie Deebo
Testo della canzone Akumbutseni (Emmie Deebo), tratta dall'album First Born
Its Macia, the rhythm boy. Deebo!
Amatinena kuti ndife olowelela
Kungotiwona ati tilibe nzelu
Poti samamwa mowa, samaminula, amadzitcha Che Good
Ife tikangomwako, kuvala bwino ati tili m'ziwanda
Chonsecho mumtima mwao muli njoka yolusa adonawa!
Mwadzadza kaduka mkwiyo kukhomelela anzao khathikhathi!
Chonsencho mu mtima mwawo muli moto olusa amkolo!
Kumangoti bola atamike ku mpingo kugulu awoneke m'ngelo ooh!
Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Asanaweluze Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Asanaweluze Akumbutseni
Aaaa Akumbutseni
Asanayambe kuchotsa chanzawo
Aaa Akumbutseni
Ayambe kuchotsa chawo oh!
Aaa Akumbutseni
Asiye kujama yanzawo
Aaa Akumbutseni
Eyeee eee!
Kuchita kulawilila,
Ati mwana wanu Mayi akusochela
Zomwe apangazi khulupilani tsiku lina m'dzalila
Ooh! Ayiwala, ali ndi ana awo osochela
M'malo mokonza awo, ali likiliki kuweluza ena aaa!
Aiwala ali ndi moyo wawo awusamale
Koma kuzonda amzawo akuyenda bwanji, akupanga chani?
Ooh afuna tizifinyika
Afuna tiziwaopa
Afuna tizibanika
Ngati amatisunga ndiwowa!
Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Asanaweluze Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Asanaweluze Akumbutseni
Aaaa Akumbutseni
Asanayambe kuchotsa chanzawo
Aaa Akumbutseni
Ayambe kuchotsa chawo oh!
Aaa Akumbutseni
Asiye kujama yanzawo
Aaa Akumbutseni
Eyeee eeeh!
Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Asanaweluze Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Akumbutseni
Asanaweluze Akumbutseni
Aaaa Akumbutseni
Asanayambe kuchotsa chanzawo
Aaa Akumbutseni
Ayambe kuchotsa chawo oh!
Aaa Akumbutseni
Asiye kujama yanzawo
Aaa Akumbutseni
Credits
Writer(s): Emily Zintambira
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
Disclaimer:
i testi sono forniti da Musixmatch.
Per richieste di variazioni o rimozioni è possibile contattare
direttamente Musixmatch nel caso tu sia
un artista o
un publisher.