Testo Malire - Emmie Deebo
Testo della canzone Malire (Emmie Deebo), tratta dall'album First Born
I may never be the missing voice
Luso langa lili incomplete
Ati mwaine mulibe golide I'm a me e ss
Ati kumwamba kulibeko malo anga
Ndungotaya nthawi yanga
Poti ndinaotcha kachisi ndimachimo
Zatengela kulimba mtima
Ndipo singachitile mwina
Poti ndayenela kudza chifupi Nanu!
Oh! ooh!
Komwe ndachoka ndikutali mundilandire
Zomwe ndasenza ndizambili mundilandire eh
Poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
Nde ndi Inuyo, ndi Inuyo ondiombola
Ondiombola ndani? (Ndi Inuyo, ndi Inuyo, ndi Inuyo)
Ondiombola ndani? (Ndi Inuyo ndi Inuyo ndi Inuyo oh)
Poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
Nde ndi Inuyo ndi Inuyo ondiombola
Kubwela pano you're my last hope!
Ndabalalika and I'm deeply so, distance
Ndilibe kothawila.
Ndeno mtima umati njenjenje oh!
Ndilibe mtendere oh Lord
Ndagwada pa mawondo
Nde ndifuna mundisambitse oh
Mumadzi amoyo onse
Mundipulumutse ooh
Komwe ndachoka ndikutali mundilandire
Zomwe ndasenza ndizambili mundilandire eh
Poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
Nde ndi Inuyo, ndi Inuyo ondiombola
Ondiombola ndani? (Ndi Inuyo, ndi Inuyo, ndi Inuyo)
Ondiombola ndani? (Ndi Inuyo ndi Inuyo ndi Inuyo oh)
Poti sindingasunthe anthuwa andilembela malire
Nde ndi Inuyo ndi Inuyo ondiombola
Credits
Writer(s): Emily Zintambira
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
Disclaimer:
i testi sono forniti da Musixmatch.
Per richieste di variazioni o rimozioni è possibile contattare
direttamente Musixmatch nel caso tu sia
un artista o
un publisher.