Testo Vuto - Ritaa
Testo della canzone Vuto (Ritaa), tratta dall'album Vuto
Nkhawa yandigwira (I am stressed)
Mnyumba mwa anzanga, ana Mpaka akula
(In my mates houses, the children are grown)
Chomwe ndingamange, chingomasuka (What I tie, gets untied)
Ndingaumbe, chingogumuka (What I make, it breaks
Ndingatole, chingotaika (What I pick, it drops)
Anthu akundiseka ine (They are laughing at me
Akuti undisiya ine (They say you'll leave me)
Upeza wina iwe (You'll find another)
Anthu akundiseka ine (They are laughing at me)
Akuti undisiya ine (They say you'll leave me)
Upeza wina iwe (You'll find another)
Mwina vuto ndi ine (Maybe I am the problem)
Vuto ndi ine, vuto ndi ine
Vuto ndi ine, vuto ndi ine
Amati akulu ndiye m'dambo (They say elders are a pond)
Mozimira moto (That quenches fires)
Ndipatseni malangizo (Tell me what to do)
Mukuti yesabe, yesabe (You say keep trying)
Komabe, komabe (But still, but still)
Chitonzo changa chagwera pa mwana (My problem is a child)
Anthu akundiseka ine (They are laughing at me
Akuti undisiya ine (They say you'll leave me)
Upeza wina iwe (You'll find another)
Anthu akundiseka ine (They are laughing at me)
Akuti undisiya ine (They say you'll leave me)
Upeza wina iwe (You'll find another)
Mwina vuto ndi ine (Maybe I am the problem)
Vuto ndi ine, Vuto ndi ine
Vuto ndi ine, Vuto ndi ine
Mwina vuto si ine (But maybe I am not the problem)
Hey (But maybe Iam not the problem)
Credits
Writer(s): Rita Mwantalli
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
Disclaimer:
i testi sono forniti da Musixmatch.
Per richieste di variazioni o rimozioni è possibile contattare
direttamente Musixmatch nel caso tu sia
un artista o
un publisher.