Testo Desperate - Teddy Music
Testo della canzone Desperate (Teddy Music), tratta dall'album MAKADI
M'ma
Makadidido eeh
Oh yeah, oh yeah, ooh yeah
I know it's not okay
Kuti nthawi zonse nzikukulonda iwe
Baby I can't help it
I still believe the odds will play in my favour
Do you think of me?
Olo mwina zoti ndakusowa iweyo
Nthawi yonseyi
Ndinkaganiza zoti sungagwidwe
Kapena mwina m'minyama ah
Zoti unandithawa ah
Pano yatsala ndi nkhawa ah
Iwe sunkandikonda ah
Kodi unandinamiza? ah
When you told me love always wins
Ine ndimanva kuwawa
Daily nkama ku stalker ah
I know it's not okay
It's not okay
It's not okay
It's not okay
Baby I am desperate
I am desperate
I am desperate
I am desperate
Ma ine, ma ine
Daily m'mangoganiza za iwe
Anzanga nawo amathoka za iwe
Anzako nawo akuti you're happy iwe
Nnaziyambilanji za chikondi izi?
Zanga zimangothela misonzi
Why do you look better and excited?
Zaka zonsezi sunawonekepo chonchi iwe
Kapena mwina m'minyama ah
Zoti unandithawa ah
Pano yatsala ndi nkhawa ah
Iwe sunkandikonda ah
Kodi unandinamiza? ah
When you told me love always wins
Ine ndimanva kuwawa
Daily nkama ku stalker and
I know it's not okay
It's not okay
It's not okay
It's not okay
Baby I am desperate
I am desperate
I am desperate
I am desperate
Kapena mwina m'minyama ah
Zoti unandithawa ah
Pano yatsala ndi nkhawa ah
Iwe sunkandikonda ah
Kodi unandinamiza? ah
When you told me love always wins
Ine ndimanva kuwawa
Daily nkama ku stalker ah
Credits
Writer(s): Teddy Maliza
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Link
Disclaimer:
i testi sono forniti da Musixmatch.
Per richieste di variazioni o rimozioni è possibile contattare
direttamente Musixmatch nel caso tu sia
un artista o
un publisher.